Chivumbulutso 21:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Mpandawo unamangidwa ndi mwala wa yasipi+ ndipo mzindawo unamangidwa ndi golide woyenga bwino woonekera ngati galasi. Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 21:18 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 307-308
18 Mpandawo unamangidwa ndi mwala wa yasipi+ ndipo mzindawo unamangidwa ndi golide woyenga bwino woonekera ngati galasi.