-
Chivumbulutso 21:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Maziko a mpanda wa mzindawo anawakongoletsa ndi miyala yamtengo wapatali ya mitundu yosiyanasiyana: maziko oyamba anali amwala wa yasipi, achiwiri wa safiro, achitatu wa kalikedo, a 4 wa emarodi,
-