Chivumbulutso 22:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mulungu sadzatembereranso mzindawo. Koma mpando wachifumu wa Mulungu ndi wa Mwanawankhosa+ udzakhala mumzindamo ndipo akapolo a Mulungu adzachita utumiki wopatulika kwa iye. Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 22:3 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 312-313
3 Mulungu sadzatembereranso mzindawo. Koma mpando wachifumu wa Mulungu ndi wa Mwanawankhosa+ udzakhala mumzindamo ndipo akapolo a Mulungu adzachita utumiki wopatulika kwa iye.