Chivumbulutso 22:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iye anandiuza kuti: “Mawu awa ndi odalirika ndiponso oona.+ Yehova,* Mulungu amene anauzira aneneri+ kuti apereke mauthenga, watumiza mngelo wake kuti adzaonetse akapolo ake zinthu zimene zikuyenera kuchitika posachedwa. Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 22:6 Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 314 Nsanja ya Olonda,12/1/1999, tsa. 19
6 Iye anandiuza kuti: “Mawu awa ndi odalirika ndiponso oona.+ Yehova,* Mulungu amene anauzira aneneri+ kuti apereke mauthenga, watumiza mngelo wake kuti adzaonetse akapolo ake zinthu zimene zikuyenera kuchitika posachedwa.