-
Chivumbulutso 22:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Ine Yohane, ndi amene ndinamva komanso kuona zinthu zimenezi. Nditamva komanso kuona zinthu zimenezi, ndinagwada nʼkuwerama pamapazi a mngelo amene ankandionetsa zinthu zimenezi kuti ndimulambire.
-