Chivumbulutso 22:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma iye anandiuza kuti: “Samala! Usachite zimenezo! Inetu ndangokhala kapolo mnzako, kapolo wa aneneri amene ndi abale ako komanso wa anthu amene akutsatira mawu amumpukutu umenewu. Lambira Mulungu.”+ Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 22:9 Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 314 Nsanja ya Olonda,8/1/1999, tsa. 14
9 Koma iye anandiuza kuti: “Samala! Usachite zimenezo! Inetu ndangokhala kapolo mnzako, kapolo wa aneneri amene ndi abale ako komanso wa anthu amene akutsatira mawu amumpukutu umenewu. Lambira Mulungu.”+