Chivumbulutso 22:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Osangalala ndi amene achapa mikanjo yawo+ kuti akhale ndi ufulu wodya zipatso zamʼmitengo ya moyo,+ ndiponso kuti aloledwe kulowa mumzindawo kudzera pamageti ake.+ Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 22:14 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),9/2018, tsa. 20 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 316-317
14 Osangalala ndi amene achapa mikanjo yawo+ kuti akhale ndi ufulu wodya zipatso zamʼmitengo ya moyo,+ ndiponso kuti aloledwe kulowa mumzindawo kudzera pamageti ake.+