Chivumbulutso 22:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “Ine ndikuchitira umboni kwa aliyense amene wamva mawu a ulosi wamumpukutuwu kuti: Wina akawonjezera pa zimenezi,+ Mulungu adzamuwonjezera miliri imene yalembedwa mumpukutuwu.+ Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 22:18 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 318-319
18 “Ine ndikuchitira umboni kwa aliyense amene wamva mawu a ulosi wamumpukutuwu kuti: Wina akawonjezera pa zimenezi,+ Mulungu adzamuwonjezera miliri imene yalembedwa mumpukutuwu.+