Chivumbulutso 22:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndipo wina akachotsa kalikonse pa mawu amumpukutu wa ulosi umenewu, Mulungu adzachotsa gawo lake pa zimene zalembedwa mumpukutuwu. Kutanthauza kuti sadzamulola kudya zipatso zamʼmitengo ya moyo+ komanso sadzamulola kulowa mumzinda woyerawo.+ Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 22:19 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 318-319
19 Ndipo wina akachotsa kalikonse pa mawu amumpukutu wa ulosi umenewu, Mulungu adzachotsa gawo lake pa zimene zalembedwa mumpukutuwu. Kutanthauza kuti sadzamulola kudya zipatso zamʼmitengo ya moyo+ komanso sadzamulola kulowa mumzinda woyerawo.+