Genesis 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Dziko lapansi linali lopanda maonekedwe enieni ndiponso lopanda kanthu. Panali madzi akuya+ kwambiri ndipo pamwamba pake panali mdima wokhawokha. Ndipo mphamvu* ya Mulungu inali kuyendayenda+ pamwamba pa madzi akuyawo.+ Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:2 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo, Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 6 Galamukani!,No. 3 2021 tsa. 10 Nsanja ya Olonda,2/15/2007, ptsa. 5-6
2 Dziko lapansi linali lopanda maonekedwe enieni ndiponso lopanda kanthu. Panali madzi akuya+ kwambiri ndipo pamwamba pake panali mdima wokhawokha. Ndipo mphamvu* ya Mulungu inali kuyendayenda+ pamwamba pa madzi akuyawo.+
1:2 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo, Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 6 Galamukani!,No. 3 2021 tsa. 10 Nsanja ya Olonda,2/15/2007, ptsa. 5-6