Genesis 1:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndiyeno Mulungu anati: “Dziko lapansi limere udzu, limere zomera zobala mbewu,+ limere mitengo yobala zipatso zokhala ndi mbewu yake, monga mwa mtundu wake.”+ Ndipo zinaterodi. Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:11 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo, Galamukani!,3/2014, tsa. 7 Nsanja ya Olonda,2/15/2007, tsa. 6
11 Ndiyeno Mulungu anati: “Dziko lapansi limere udzu, limere zomera zobala mbewu,+ limere mitengo yobala zipatso zokhala ndi mbewu yake, monga mwa mtundu wake.”+ Ndipo zinaterodi.