Genesis 34:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 “Anthu awa n’ngofuna mtendere ndi ife.+ Ndiye aloleni akhale m’dzikoli ndi kuchitamo malonda, popeza dzikoli n’lalikulu moti atha kukhalamo.+ Tikhoza kukwatira ana awo aakazi, ndiponso tikhoza kuwapatsa ana athu aakazi.+
21 “Anthu awa n’ngofuna mtendere ndi ife.+ Ndiye aloleni akhale m’dzikoli ndi kuchitamo malonda, popeza dzikoli n’lalikulu moti atha kukhalamo.+ Tikhoza kukwatira ana awo aakazi, ndiponso tikhoza kuwapatsa ana athu aakazi.+