-
Genesis 34:24Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
24 Chotero anthu onse otuluka pachipata cha mzindawo anamvera Hamori ndi mwana wake Sekemu, ndipo amuna onse a mumzinda wakewo anadulidwa.
-