Genesis 34:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Anaphanso Hamori ndi mwana wake Sekemu ndi lupanga.+ Kenako anatenga Dina m’nyumba ya Sekemu, n’kupita naye.+
26 Anaphanso Hamori ndi mwana wake Sekemu ndi lupanga.+ Kenako anatenga Dina m’nyumba ya Sekemu, n’kupita naye.+