Genesis 34:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ana ena a Yakobo anamalizitsa amuna omwe anali atapwetekedwa koopsa, n’kutenga katundu yense wa mumzindamo. Anatero chifukwa anthuwo anagwiririra mlongo wawo.+
27 Ana ena a Yakobo anamalizitsa amuna omwe anali atapwetekedwa koopsa, n’kutenga katundu yense wa mumzindamo. Anatero chifukwa anthuwo anagwiririra mlongo wawo.+