Genesis 39:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Tsopano Yosefe uja, Aisimaeli+ anapita naye ku Iguputo,+ ndipo kumeneko anakam’gulitsa kwa Potifara.+ Potifara anali Mwiguputo, yemwe anali nduna ya panyumba ya Farao, komanso mkulu wa asilikali olondera mfumu. Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 39:1 Nsanja ya Olonda,11/1/2014, ptsa. 12-13
39 Tsopano Yosefe uja, Aisimaeli+ anapita naye ku Iguputo,+ ndipo kumeneko anakam’gulitsa kwa Potifara.+ Potifara anali Mwiguputo, yemwe anali nduna ya panyumba ya Farao, komanso mkulu wa asilikali olondera mfumu.