Genesis 39:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Atatero, anasunga malaya a mnyamatayo pambali pake kufikira mwamuna wake atabwera kunyumbako.+