Genesis 40:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mmenemo, mkulu wa asilikali olondera mfumu anaika Yosefe kuti azikhala nawo n’kumawalondera,+ ndipo iwo anakhala m’ndendemo kwa masiku ndithu.
4 Mmenemo, mkulu wa asilikali olondera mfumu anaika Yosefe kuti azikhala nawo n’kumawalondera,+ ndipo iwo anakhala m’ndendemo kwa masiku ndithu.