Genesis 40:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Komabe, zonse zikadzakhala bwino kwa iwe usadzandiiwale.+ Chonde, udzandikomere mtima ponditchula kwa Farao,+ ndipo ukayesetse kuti ndidzatuluke m’ndende muno. Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 40:14 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),4/2017, ptsa. 20-21
14 Komabe, zonse zikadzakhala bwino kwa iwe usadzandiiwale.+ Chonde, udzandikomere mtima ponditchula kwa Farao,+ ndipo ukayesetse kuti ndidzatuluke m’ndende muno.