Genesis 5:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Mwanayo anamutcha dzina lakuti Nowa,+ ndipo anati: “Uyu ndi amene adzatibweretsere mpumulo ku ntchito yathu yopweteketsa manja, chifukwa cholima nthaka imene Yehova anaitemberera.”+ Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:29 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),6/2017, tsa. 8 Nsanja ya Olonda,4/1/2013, tsa. 142/1/2009, tsa. 1311/15/2001, tsa. 2911/1/1996, tsa. 8 Tsanzirani, tsa. 22
29 Mwanayo anamutcha dzina lakuti Nowa,+ ndipo anati: “Uyu ndi amene adzatibweretsere mpumulo ku ntchito yathu yopweteketsa manja, chifukwa cholima nthaka imene Yehova anaitemberera.”+
5:29 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),6/2017, tsa. 8 Nsanja ya Olonda,4/1/2013, tsa. 142/1/2009, tsa. 1311/15/2001, tsa. 2911/1/1996, tsa. 8 Tsanzirani, tsa. 22