Genesis 45:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pamenepo Yosefe anauza abale akewo kuti: “Senderani pafupi ndi ine.” Ndipo anasenderadi pafupi naye. Ndiyeno Yosefe anati: “Ndine m’bale wanu uja Yosefe, amene munamugulitsa ku Iguputo.+
4 Pamenepo Yosefe anauza abale akewo kuti: “Senderani pafupi ndi ine.” Ndipo anasenderadi pafupi naye. Ndiyeno Yosefe anati: “Ndine m’bale wanu uja Yosefe, amene munamugulitsa ku Iguputo.+