Genesis 45:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Inuyo, ana anu, adzukulu anu, nkhosa ndi ng’ombe zanu, ndi zonse zimene muli nazo mudzakhale m’dziko la Goseni+ pafupi ndi ine.
10 Inuyo, ana anu, adzukulu anu, nkhosa ndi ng’ombe zanu, ndi zonse zimene muli nazo mudzakhale m’dziko la Goseni+ pafupi ndi ine.