Genesis 45:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Yosefe atatero, anakumbatira Benjamini m’bale wake n’kuyamba kulira. Nayenso Benjamini analira atakumbatira m’bale wakeyo.+
14 Yosefe atatero, anakumbatira Benjamini m’bale wake n’kuyamba kulira. Nayenso Benjamini analira atakumbatira m’bale wakeyo.+