Genesis 45:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndiyeno Farao anauza Yosefe kuti: “Uza abale ako kuti, ‘Chitani izi: Kwezani katundu panyama zanu, mupite kudziko la Kanani.+
17 Ndiyeno Farao anauza Yosefe kuti: “Uza abale ako kuti, ‘Chitani izi: Kwezani katundu panyama zanu, mupite kudziko la Kanani.+