Genesis 45:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Uwauzenso kuti:+ “Chitani izi: Mutenge ngolo+ kuno ku Iguputo zokatengera ana anu aang’ono ndi akazi anu. Ngolo ina mukatengere bambo anu n’kubwera kuno.+
19 Uwauzenso kuti:+ “Chitani izi: Mutenge ngolo+ kuno ku Iguputo zokatengera ana anu aang’ono ndi akazi anu. Ngolo ina mukatengere bambo anu n’kubwera kuno.+