Genesis 45:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ana a Isiraeli aja anachitadi zimenezo. Yosefe anawapatsa ngolo monga momwe Farao analamulira. Anawapatsanso kamba+ wa pa ulendo.
21 Ana a Isiraeli aja anachitadi zimenezo. Yosefe anawapatsa ngolo monga momwe Farao analamulira. Anawapatsanso kamba+ wa pa ulendo.