Genesis 45:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Pamenepo Isiraeli anafuula kuti: “Basi, tsopano ndakhulupirira! Yosefe mwana wanga akadali ndi moyo! Ndipita ndikamuone ndisanafe!”+
28 Pamenepo Isiraeli anafuula kuti: “Basi, tsopano ndakhulupirira! Yosefe mwana wanga akadali ndi moyo! Ndipita ndikamuone ndisanafe!”+