Genesis 6:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 M’kupita kwa nthawi, Nowa anabereka ana aamuna atatu, Semu, Hamu ndi Yafeti.+