Genesis 6:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Udzalowetsenso m’chingalawacho chamoyo chilichonse cha mtundu uliwonse.+ Udzazilowetse ziwiriziwiri, champhongo ndi chachikazi, kuti zidzasungike zamoyo limodzi nawe.+ Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:19 Nsanja ya Olonda,8/1/2013, ptsa. 13-14
19 Udzalowetsenso m’chingalawacho chamoyo chilichonse cha mtundu uliwonse.+ Udzazilowetse ziwiriziwiri, champhongo ndi chachikazi, kuti zidzasungike zamoyo limodzi nawe.+