Genesis 7:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pa tsiku limeneli Nowa analowa m’chingalawacho. Analowa limodzi ndi ana ake, Semu, Hamu ndi Yafeti,+ ndiponso mkazi wake, ndi akazi atatu a ana akewo.+
13 Pa tsiku limeneli Nowa analowa m’chingalawacho. Analowa limodzi ndi ana ake, Semu, Hamu ndi Yafeti,+ ndiponso mkazi wake, ndi akazi atatu a ana akewo.+