Genesis 7:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Chotero zamoyo zonse zoyenda padziko lapansi, monga zolengedwa zouluka, nyama zoweta, nyama zakutchire, ndiponso tizilombo tonse tambirimbiri toyenda padziko lapansi, zinafa+ pamodzi ndi anthu onse.+
21 Chotero zamoyo zonse zoyenda padziko lapansi, monga zolengedwa zouluka, nyama zoweta, nyama zakutchire, ndiponso tizilombo tonse tambirimbiri toyenda padziko lapansi, zinafa+ pamodzi ndi anthu onse.+