Genesis 8:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pambuyo pake, Mulungu anakumbukira+ Nowa ndi nyama zonse zakutchire, ndiponso nyama zonse zoweta zimene anali nazo m’chingalawa.+ Ndiyeno Mulungu anachititsa chimphepo kuwomba padziko lapansi, ndipo madzi anayamba kuchepa.+
8 Pambuyo pake, Mulungu anakumbukira+ Nowa ndi nyama zonse zakutchire, ndiponso nyama zonse zoweta zimene anali nazo m’chingalawa.+ Ndiyeno Mulungu anachititsa chimphepo kuwomba padziko lapansi, ndipo madzi anayamba kuchepa.+