Genesis 8:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pamenepo, akasupe a madzi akuya+ ndi zotsekera madzi+ akumwamba zinatsekeka, choncho madzi omwe anali kukhuthuka kuchokera kumwamba anasiya.
2 Pamenepo, akasupe a madzi akuya+ ndi zotsekera madzi+ akumwamba zinatsekeka, choncho madzi omwe anali kukhuthuka kuchokera kumwamba anasiya.