Genesis 8:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndiyeno patatha masiku 40, Nowa anatsegula windo+ la chingalawa limene anaika.