Genesis 8:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Anadikirabe masiku enanso 7. Kenako anaitumizanso njiwa ija, koma sinabwererenso kwa iye.+