Genesis 8:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Tsopano Nowa anamangira Yehova guwa lansembe.+ Atatero, anatenga zina mwa nyama zonse zoyera,+ ndi zina mwa zouluka zonse zoyera,+ n’kuzipereka nsembe yopsereza paguwapo.+ Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:20 Nsanja ya Olonda,8/1/2013, tsa. 15
20 Tsopano Nowa anamangira Yehova guwa lansembe.+ Atatero, anatenga zina mwa nyama zonse zoyera,+ ndi zina mwa zouluka zonse zoyera,+ n’kuzipereka nsembe yopsereza paguwapo.+