Genesis 1:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Motero Mulungu anapanga nyama zakutchire monga mwa mitundu yake. Anapanganso nyama zoweta monga mwa mitundu yake, komanso nyama iliyonse yokwawa panthaka monga mwa mtundu wake.+ Ndipo Mulungu anaona kuti zili bwino. Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:25 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 6 Mawu a Mulungu, ptsa. 94-95 Nsanja ya Olonda,4/1/1986, ptsa. 13-14
25 Motero Mulungu anapanga nyama zakutchire monga mwa mitundu yake. Anapanganso nyama zoweta monga mwa mitundu yake, komanso nyama iliyonse yokwawa panthaka monga mwa mtundu wake.+ Ndipo Mulungu anaona kuti zili bwino.
1:25 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 6 Mawu a Mulungu, ptsa. 94-95 Nsanja ya Olonda,4/1/1986, ptsa. 13-14