Genesis 12:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pamenepo, Abulamu ananyamuka malinga ndi mmene Yehova anamuuzira, ndipo Loti ananyamuka naye limodzi. Pochoka ku Harana,+ Abulamu anali ndi zaka 75. Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:4 Nsanja ya Olonda,8/15/2001, tsa. 17
4 Pamenepo, Abulamu ananyamuka malinga ndi mmene Yehova anamuuzira, ndipo Loti ananyamuka naye limodzi. Pochoka ku Harana,+ Abulamu anali ndi zaka 75.