Genesis 12:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iye anatenga mkazi wake Sarai,+ Loti mwana wa m’bale wake,+ ndi chuma chawo chonse,+ komanso akapolo awo onse amene anapeza kudziko la Harana. Iwo ananyamuka ulendo wopita kudziko la Kanani.+ Potsirizira pake anafika ku Kanani. Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:5 Nsanja ya Olonda (Yogawira),No. 3 2017, tsa. 14 Tsanzirani, tsa. 30 Nsanja ya Olonda,8/15/2001, tsa. 17 Galamukani!,7/8/1988, tsa. 29
5 Iye anatenga mkazi wake Sarai,+ Loti mwana wa m’bale wake,+ ndi chuma chawo chonse,+ komanso akapolo awo onse amene anapeza kudziko la Harana. Iwo ananyamuka ulendo wopita kudziko la Kanani.+ Potsirizira pake anafika ku Kanani.
12:5 Nsanja ya Olonda (Yogawira),No. 3 2017, tsa. 14 Tsanzirani, tsa. 30 Nsanja ya Olonda,8/15/2001, tsa. 17 Galamukani!,7/8/1988, tsa. 29