8 M’kupita kwa nthawi, anasamuka pamalopo n’kupita kudera lamapiri, kum’mawa kwa Beteli.+ Kumeneko iye anamanga hema wake. Beteli anali kumadzulo kwake ndipo Ai+ anali kum’mawa kwake. Kenako anamangira Yehova guwa lansembe,+ n’kuyamba kuitana pa dzina la Yehova.+