-
Genesis 12:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Aiguputo akakuona, mosakayikira anena kuti, ‘Ameneyu ndi mkazi wake.’ Ndipo andipha ndithu, koma iweyo akusiya wamoyo.
-