Genesis 13:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Abulamu anali ndi chuma chambiri. Anali ndi ziweto, siliva ndi golide.+