Genesis 13:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kenako Abulamu anachoka ku Negebu. Anali kumanga misasa ndi kusamuka mpaka kukafika ku Beteli, kumene kunali hema wake poyamba, pakati pa Beteli ndi Ai.+ Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:3 Nsanja ya Olonda (Yogawira),No. 5 2017, tsa. 12 Nsanja ya Olonda,8/15/2001, tsa. 21
3 Kenako Abulamu anachoka ku Negebu. Anali kumanga misasa ndi kusamuka mpaka kukafika ku Beteli, kumene kunali hema wake poyamba, pakati pa Beteli ndi Ai.+