Genesis 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Golide wa dziko limenelo ndi wabwino.+ Kulinso mafuta onunkhira a bedola+ ndi miyala yamtengo wapatali ya onekisi.+ Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:12 Nsanja ya Olonda,8/1/1989, ptsa. 12-15
12 Golide wa dziko limenelo ndi wabwino.+ Kulinso mafuta onunkhira a bedola+ ndi miyala yamtengo wapatali ya onekisi.+