Genesis 19:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma iwo asanagone, amuna a mumzindamo, amuna a mu Sodomu, anafika n’kuzungulira nyumbayo.+ Anafika ali chigulu, kuyambira tianyamata mpaka nkhalamba.+ Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:4 Galamukani!,10/8/1993, tsa. 3
4 Koma iwo asanagone, amuna a mumzindamo, amuna a mu Sodomu, anafika n’kuzungulira nyumbayo.+ Anafika ali chigulu, kuyambira tianyamata mpaka nkhalamba.+