Genesis 19:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndiyeno alendowo anafunsa Loti kuti: “Kodi uli ndi achibale alionse kuno? Uwatulutse mumzinda uno,+ kaya ndi akamwini ako, ana ako aamuna, ana ako aakazi, kapena alionse amene ndi abale ako. Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:12 Nsanja ya Olonda,4/15/1990, ptsa. 17-18
12 Ndiyeno alendowo anafunsa Loti kuti: “Kodi uli ndi achibale alionse kuno? Uwatulutse mumzinda uno,+ kaya ndi akamwini ako, ana ako aamuna, ana ako aakazi, kapena alionse amene ndi abale ako.