Genesis 19:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Malo ano tiwawononga chifukwa kudandaula kokhumudwa ndi anthuwa kwamveka kwambiri kwa Yehova,+ moti Yehova watituma kudzawononga mzindawu.”+
13 Malo ano tiwawononga chifukwa kudandaula kokhumudwa ndi anthuwa kwamveka kwambiri kwa Yehova,+ moti Yehova watituma kudzawononga mzindawu.”+