Genesis 19:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Atafika nawo kunja kwa mzinda, mmodzi wa iwo anati: “Thawani mupulumutse moyo wanu!+ Musacheukire kumbuyo+ ndipo musaime chilili pamalo alionse m’Chigawochi.*+ Thawirani kudera la kumapiri kuti musawonongedwe!”+
17 Atafika nawo kunja kwa mzinda, mmodzi wa iwo anati: “Thawani mupulumutse moyo wanu!+ Musacheukire kumbuyo+ ndipo musaime chilili pamalo alionse m’Chigawochi.*+ Thawirani kudera la kumapiri kuti musawonongedwe!”+