Genesis 19:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Chonde taonani pali mzinda waung’ono+ pafupipa umene ndingathawireko. Zimene ndikukupemphanizi si nkhani yaing’ono kodi? Chonde ndiloleni ndithawire kumzinda umenewo. Ndikatero, moyo wanga upulumuka.”+
20 Chonde taonani pali mzinda waung’ono+ pafupipa umene ndingathawireko. Zimene ndikukupemphanizi si nkhani yaing’ono kodi? Chonde ndiloleni ndithawire kumzinda umenewo. Ndikatero, moyo wanga upulumuka.”+