Genesis 21:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Isaki atakwanitsa masiku 8, Abulahamu anamudula mwana wakeyo, monga mmene Mulungu anamulamulira.+